Sewero la Mfumu Edipa
ANTHU A M’SEWEROLI
EDIPA: Mfumu ya ku Thebesi
WANSEMBE: Mkulu wansembe wa ku Thebesi
KIREYO: Mlamu wa Edipa
GULU LA ANTHU: Akuluakulu a ku Thebesi
TERESI: Mneneri wachikulire yemwe ndi wosawona
MNYAMATA: Munthu wotsogolera Teresi
YOKASI: Mkazi wa Edipa, mchemwali wa Kireyo
NTHENGA: Munthu wachikulire
WANTCHITO: M’busa wachikulire
WANTCHITO WACHIWIRI: Mtumiki wa Edipa
ANTIGONE: Mwana wamkazi wa Edipa ndi Yokasi
ISIMENE: Mwana wamkazi wa Edipa ndi Yokasi
1