Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 311
Paphata pa Chichewa
Nzangwali: Munthu wamtali kwambiri.
Chitsanzo: (1) Mwanayu ndi nzangwali. (2) Anthu ambiri
amene amakhala m’madera a mango amakhala
azangwali.
Nzeruzayekha: Munthu wosamva zonena za anzake.
Chitsanzo: Alikuti nzeruzayekha uja?
Nzika: Munthu yemwe wakhalitsa m’dziko.
Chitsanzo: Ine ndi nzika ya dziko lino.
310