Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Miyambi ya Patsokwe | Page 18

Miyambi ya Patsokwe Awonenji adapha njovu ndi mbuna. -Munthu aliyense ali ndi mwayi wake. Choncho, si bwino ku- ganiza kuti anthu ena ooneka onyozeka sangapeze mwayi. 17