Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Matigari | Page 4
Matigari
Chifukwa cha umphawi komanso mavuto, anthu oponde-
rezedwawo amayamba kuchita zoipa zomwe zimachititsa kuti
dzanja la lamulo liwagwire. Koma olamulirawo kapena olemera
akalakwa, amatha kumangochita zoipa ali neng’a pachimpando
chawofuwofu ndipo sachitidwa chilichonse. Pomwe wosauka
akaba nkhuku kapena kuchita zimene olamulirawo sakugwiri-
zana nazo, amakawolera kundende.
The Series of Rodgers Bounty Books [RBB]
Copyright © January 2014 by Bonwell “Kadyankena” Rodgers.
All rights reserved. No part of this publication may be reproduced or transmitted in any form or by any means, electronical or mechanical, including
photocopy, recording or any imformation storage and retrieval system, without permission in writing from the owner.
Requests for permission should be mailed to: [email protected]
Phone: 0881813953, 0881831435
3