Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Paphata pa Chichewa | Page 22
Paphata pa Chichewa
Bzola: Kuposa, kupitirira.
Chitsanzo: Mavuto sangabzole apa.
Balamutsa: Thamangitsa mwachipongwe.
Chitsanzo: Anawabalamutsako kwa abale awo kuja
chifukwa cha dyera.
21