Agoloso Presents - Atondido Stories Agoloso Presents - Matigari | Page 141
Matigari
Iye anaganiza kuti: “Zikanakhala bwino kukanangogwa
mvula kapena kuwala dzuwa kusiyana ndi nyengo yosadziwika
bwino yomwe ili leroyi. Inde, zikanakhala bwino kukanatentha
kapena kuzizira, m’malo mongokhala ndi nyengo yosadziwika
bwinobwino.
Kenako anauyamba wopita kukafunafuna anthu anzeru om-
we amaphunzitsa komanso omwe anaphunzira nyenyezi za-
makono.
140